Aroma 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tikudziwa kuti popeza Khristu waukitsidwa,+ sadzafanso+ ndipo imfa sikumulamuliranso ngati mfumu.