Aroma 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Popeza pamene tinali ofooka,+ Khristu anafera anthu osapembedza Mulungu pa nthawi yoikidwiratu.+ 1 Petulo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pajatu ngakhale Khristu anafera machimo kamodzi kokha basi.+ Munthu wolungamayo anafera anthu osalungama,+ kuti akufikitseni kwa Mulungu.+ Iye anaphedwa m’thupi,+ koma anaukitsidwa monga mzimu.+
18 Pajatu ngakhale Khristu anafera machimo kamodzi kokha basi.+ Munthu wolungamayo anafera anthu osalungama,+ kuti akufikitseni kwa Mulungu.+ Iye anaphedwa m’thupi,+ koma anaukitsidwa monga mzimu.+