Mateyu 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mofanana ndi zimenezi, Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa, koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuwombola anthu ambiri.”+
28 Mofanana ndi zimenezi, Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa, koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuwombola anthu ambiri.”+