Luka 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kodi wamkulu ndani, amene akudya patebulo kapena amene akutumikira? Si amene akudya patebulo kodi? Koma ine ndili pakati panu monga wotumikira.+ Yohane 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho ngati ine, wokhala Ambuye ndi Mphunzitsi, ndasambitsa mapazi anu,+ inunso muyenera kusambitsana mapazi.+ Afilipi 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sanatero ayi, koma anasiya zonse zimene anali nazo n’kukhala ngati kapolo,+ ndi kukhala wofanana ndi anthu.+
27 Kodi wamkulu ndani, amene akudya patebulo kapena amene akutumikira? Si amene akudya patebulo kodi? Koma ine ndili pakati panu monga wotumikira.+
14 Choncho ngati ine, wokhala Ambuye ndi Mphunzitsi, ndasambitsa mapazi anu,+ inunso muyenera kusambitsana mapazi.+
7 Sanatero ayi, koma anasiya zonse zimene anali nazo n’kukhala ngati kapolo,+ ndi kukhala wofanana ndi anthu.+