Mateyu 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mofanana ndi zimenezi, Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa, koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuwombola anthu ambiri.”+ Yohane 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho anaimirira pa chakudya chamadzulocho ndi kuvula malaya ake akunja. Kenako anatenga thaulo ndi kumanga m’chiuno mwake.+ Afilipi 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sanatero ayi, koma anasiya zonse zimene anali nazo n’kukhala ngati kapolo,+ ndi kukhala wofanana ndi anthu.+
28 Mofanana ndi zimenezi, Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa, koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuwombola anthu ambiri.”+
4 Choncho anaimirira pa chakudya chamadzulocho ndi kuvula malaya ake akunja. Kenako anatenga thaulo ndi kumanga m’chiuno mwake.+
7 Sanatero ayi, koma anasiya zonse zimene anali nazo n’kukhala ngati kapolo,+ ndi kukhala wofanana ndi anthu.+