Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Amosi 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+

  • Chivumbulutso 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anafuula kuti: “Musawononge dziko lapansi, kapena nyanja, kapena mitengo, kufikira titadinda chidindo+ pamphumi+ za akapolo a Mulungu wathu.”

  • Chivumbulutso 22:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako anandiuza kuti: “Mawu awa ndi odalirika ndiponso oona.+ Yehova, Mulungu wopereka mauthenga ouziridwa+ a aneneri,+ anatumiza mngelo wake kudzaonetsa akapolo ake zinthu zimene ziyenera kuchitika posachedwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena