Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 22
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 22:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 47:1
  • +Yoh 1:29

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2012, tsa. 30

    2/15/2009, tsa. 5

    6/1/2008, ptsa. 14-15

    9/15/2002, tsa. 32

    3/1/1999, tsa. 22

    9/15/1991, ptsa. 18-19

    12/15/1990, ptsa. 10-11

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 310-311

Chivumbulutso 22:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 2:7
  • +Eze 47:12
  • +Eze 47:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2015, tsa. 27

    1/15/2012, tsa. 30

    3/1/1999, tsa. 22

    11/1/1992, tsa. 7

    9/15/1991, ptsa. 18-19

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 310-312

Chivumbulutso 22:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Zek 14:11
  • +Sl 9:7
  • +Chv 3:21
  • +Aro 1:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 312-313

Chivumbulutso 22:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 17:15; Mt 5:8
  • +Chv 14:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 312-313

Chivumbulutso 22:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 21:25
  • +Yes 60:19; 1Yo 1:5
  • +Da 7:18; Chv 3:21; 14:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2012, tsa. 30

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 313

Chivumbulutso 22:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Tit 1:2; Chv 21:5
  • +2Sa 23:2; 2Ti 3:16
  • +1Sa 3:21; Yer 37:6
  • +Chv 1:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 314

    Nsanja ya Olonda,

    12/1/1999, tsa. 19

Chivumbulutso 22:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:15; 22:20
  • +Yoh 13:17; Chv 1:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 6, 314

    Nsanja ya Olonda,

    12/1/1999, tsa. 19

Chivumbulutso 22:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 10:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 314

    Nsanja ya Olonda,

    8/1/1999, tsa. 14

Chivumbulutso 22:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yow 2:28
  • +Sl 29:2; Mt 4:10; Chv 19:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 314

    Nsanja ya Olonda,

    8/1/1999, tsa. 14

Chivumbulutso 22:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 315

Chivumbulutso 22:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 12:10
  • +2Ti 3:13; Yuda 10
  • +Aro 5:1
  • +Afi 3:16; 1Pe 1:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 315-316

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1999, tsa. 7

Chivumbulutso 22:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 40:10
  • +Ahe 11:6
  • +Sl 62:12; Miy 24:12; Yer 17:10; Aro 2:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 316-317

    Kukambitsirana, tsa. 399

Chivumbulutso 22:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 44:6; Chv 1:8; 21:6
  • +Yes 48:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2136

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 316-317

    Kukambitsirana, tsa. 399

Chivumbulutso 22:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Yo 1:7; Chv 1:3
  • +Chv 2:7
  • +Chv 21:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2018, tsa. 20

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 316-317

Chivumbulutso 22:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 23:18; Mt 7:6; Afi 3:2
  • +Aga 5:20
  • +Aef 5:5
  • +Akl 3:9; Chv 21:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 316-317

Chivumbulutso 22:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 11:10; Chv 5:5
  • +Yes 11:1; 53:2; Yer 23:5; 33:15; Aro 1:3
  • +Nu 24:17; Chv 2:28

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 317-318

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/2000, tsa. 14

    8/15/1994, tsa. 31

Chivumbulutso 22:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 22:6
  • +Chv 21:9
  • +Mt 11:28
  • +Yoh 4:14
  • +Yes 55:1; Yoh 7:37; Chv 7:17; 21:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2015, ptsa. 28-29

    12/15/2011, tsa. 25

    2/15/2010, ptsa. 14-18

    6/1/2008, ptsa. 14-15

    2/15/1998, ptsa. 18-19, 24

    9/1/1993, tsa. 32

    2/1/1992, tsa. 18

    12/15/1990, ptsa. 10-15

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 310-311, 318

    Kukambitsirana, tsa. 117

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 111-112

Chivumbulutso 22:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 4:2; 12:32; Miy 30:6; Yoh 20:30; 2Ak 11:4; Aga 1:8; 1Yo 4:3
  • +2Yo 9; Chv 15:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 318-319

Chivumbulutso 22:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 2:7; 22:2
  • +Chv 21:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 318-319

Chivumbulutso 22:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 3:11; 22:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2007, tsa. 3

    12/1/1999, tsa. 19

    12/15/1994, tsa. 24

    Tsiku la Yehova, ptsa. 156-157

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 319

Chivumbulutso 22:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 16:20; 2At 3:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 319

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 22:1Eze 47:1
Chiv. 22:1Yoh 1:29
Chiv. 22:2Chv 2:7
Chiv. 22:2Eze 47:12
Chiv. 22:2Eze 47:12
Chiv. 22:3Zek 14:11
Chiv. 22:3Sl 9:7
Chiv. 22:3Chv 3:21
Chiv. 22:3Aro 1:9
Chiv. 22:4Sl 17:15; Mt 5:8
Chiv. 22:4Chv 14:1
Chiv. 22:5Chv 21:25
Chiv. 22:5Yes 60:19; 1Yo 1:5
Chiv. 22:5Da 7:18; Chv 3:21; 14:1
Chiv. 22:6Tit 1:2; Chv 21:5
Chiv. 22:62Sa 23:2; 2Ti 3:16
Chiv. 22:61Sa 3:21; Yer 37:6
Chiv. 22:6Chv 1:1
Chiv. 22:7Chv 16:15; 22:20
Chiv. 22:7Yoh 13:17; Chv 1:3
Chiv. 22:8Mac 10:25
Chiv. 22:9Yow 2:28
Chiv. 22:9Sl 29:2; Mt 4:10; Chv 19:10
Chiv. 22:10Chv 1:3
Chiv. 22:11Da 12:10
Chiv. 22:112Ti 3:13; Yuda 10
Chiv. 22:11Aro 5:1
Chiv. 22:11Afi 3:16; 1Pe 1:15
Chiv. 22:12Yes 40:10
Chiv. 22:12Ahe 11:6
Chiv. 22:12Sl 62:12; Miy 24:12; Yer 17:10; Aro 2:6
Chiv. 22:13Yes 44:6; Chv 1:8; 21:6
Chiv. 22:13Yes 48:12
Chiv. 22:141Yo 1:7; Chv 1:3
Chiv. 22:14Chv 2:7
Chiv. 22:14Chv 21:12
Chiv. 22:15De 23:18; Mt 7:6; Afi 3:2
Chiv. 22:15Aga 5:20
Chiv. 22:15Aef 5:5
Chiv. 22:15Akl 3:9; Chv 21:8
Chiv. 22:16Yes 11:10; Chv 5:5
Chiv. 22:16Yes 11:1; 53:2; Yer 23:5; 33:15; Aro 1:3
Chiv. 22:16Nu 24:17; Chv 2:28
Chiv. 22:17Chv 22:6
Chiv. 22:17Chv 21:9
Chiv. 22:17Mt 11:28
Chiv. 22:17Yoh 4:14
Chiv. 22:17Yes 55:1; Yoh 7:37; Chv 7:17; 21:6
Chiv. 22:18De 4:2; 12:32; Miy 30:6; Yoh 20:30; 2Ak 11:4; Aga 1:8; 1Yo 4:3
Chiv. 22:182Yo 9; Chv 15:1
Chiv. 22:19Chv 2:7; 22:2
Chiv. 22:19Chv 21:2
Chiv. 22:20Chv 3:11; 22:7
Chiv. 22:21Aro 16:20; 2At 3:18
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 22:1-21

Chivumbulutso

22 Ndipo anandionetsa mtsinje wa madzi a moyo,+ oyera ngati mwala wonyezimira wa kulusitalo, ukuyenda kuchokera kumpando wachifumu wa Mulungu, ndi wa Mwanawankhosa.+ 2 Mtsinjewo unali kudutsa pakati pa msewu waukulu wa mumzindawo. Kumbali iyi ya mtsinjewo ndi kumbali inayo, kunali mitengo+ ya moyo yobala zipatso zokolola maulendo 12, ndipo inali kubala zipatso mwezi uliwonse.+ Masamba a mitengoyo anali ochiritsira mitundu ya anthu.+

3 Sikudzakhalanso temberero.+ Koma mpando wachifumu wa Mulungu+ ndi wa Mwanawankhosa+ udzakhala mumzindamo, ndipo akapolo a Mulungu adzachita utumiki wopatulika+ kwa iye. 4 Iwo adzaona nkhope yake,+ ndipo dzina lake lidzakhala pamphumi pawo.+ 5 Komanso, usiku sudzakhalakonso.+ Sadzafunikiranso kuwala kwa nyale kapena kwa dzuwa, chifukwa Yehova Mulungu adzawaunikira.+ Ndipo adzalamulira monga mafumu kwamuyaya.+

6 Kenako anandiuza kuti: “Mawu awa ndi odalirika ndiponso oona.+ Yehova, Mulungu wopereka mauthenga ouziridwa+ a aneneri,+ anatumiza mngelo wake kudzaonetsa akapolo ake zinthu zimene ziyenera kuchitika posachedwa.+ 7 Ndipo taonani! Ndikubwera mofulumira.+ Wodala ndi aliyense wosunga mawu a ulosi a mumpukutu uwu.”+

8 Ine Yohane, ndine amene ndinali kumva ndi kuona zinthu zimenezi. Ndipo nditamva ndi kuona, ndinagwada n’kuwerama kuti ndilambire+ pamapazi a mngelo amene anali kundionetsa zinthu zimenezi. 9 Koma iye anandiuza kuti: “Samala! Usatero ayi! Inetu ndangokhala kapolo mnzako, ndi wa abale ako amene ndiwo aneneri,+ ndi wa anthu amene akusunga mawu a mumpukutu umenewu. Lambira Mulungu.”+

10 Anandiuzanso kuti: “Usatsekere mawu a ulosi a mumpukutu uwu, pakuti nthawi yoikidwiratu yayandikira.+ 11 Amene akuchita zosalungama, achitebe zosalungama,+ ndipo wochita zonyansa apitirizebe kuchita zonyansazo.+ Koma wolungama+ achitebe chilungamo, ndipo woyera apitirizebe kuyeretsedwa.+

12 “‘Taonani! Ndikubwera mofulumira,+ ndipo mphoto+ ndili nayo, yoti ndipereke kwa aliyense malinga ndi ntchito yake.+ 13 Ine ndine Alefa ndi Omega,+ woyamba ndi wotsiriza, chiyambi ndi mapeto.+ 14 Odala ndiwo amene achapa mikanjo+ yawo, kuti akhale ndi ufulu wa kudya zipatso za m’mitengo ya moyo,+ ndiponso kuti akalowe mumzindawo kudzera pazipata zake.+ 15 Kunja kuli anthu amene ali ngati agalu,+ amene amachita zamizimu,+ adama,+ opha anthu, opembedza mafano, ndi aliyense wokonda kulankhula ndi kuchita zachinyengo.’+

16 “‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kudzachitira umboni zinthu izi kwa inu, kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu+ ndi mbadwa+ ya Davide. Ndinenso nthanda yonyezimira.’”+

17 Mzimu+ ndi mkwatibwi+ akunenabe kuti: “Bwera!” Aliyense wakumva anene kuti: “Bwera!”+ Aliyense wakumva ludzu abwere.+ Aliyense amene akufuna, amwe madzi a moyo kwaulere.+

18 “Ine ndikuchitira umboni kwa aliyense wakumva mawu a ulosi wa mumpukutuwu, kuti: Wina akawonjezera+ pa zimenezi, Mulungu adzamuwonjezera miliri+ yolembedwa mumpukutuwu. 19 Ndipo wina akachotsa kalikonse pa mawu a mumpukutu wa ulosi umenewu, Mulungu adzachotsa gawo lake pa zolembedwa mumpukutuwu, kutanthauza kuti sadzamulola kudya zipatso za m’mitengo ya moyo,+ ndipo sadzamulola kulowa mumzinda woyerawo.+

20 “Amene akuchitira umboni zinthu zimenezi akuti, ‘Inde, ndikubwera mofulumira.’”+

“Ame! Bwerani, Ambuye Yesu.”

21 Kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye Yesu Khristu kukhale ndi oyerawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena