Deuteronomo 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Usabweretse malipiro+ a hule kapena malipiro a galu*+ m’nyumba ya Yehova Mulungu wako kuti ukwaniritse lonjezo lililonse, chifukwa zonsezo ndi zonyansa kwa Yehova Mulungu wako. Mateyu 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Musamapatse agalu zinthu zopatulika,+ kapena kuponyera nkhumba ngale zanu, kuopera kuti zingapondeponde ngalezo+ kenako n’kutembenuka ndi kukukhadzulani. Afilipi 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chenjerani ndi agalu.+ Chenjerani ndi ochita ntchito zovulaza. Chenjerani ndi anthu amene amachita mdulidwe.+
18 Usabweretse malipiro+ a hule kapena malipiro a galu*+ m’nyumba ya Yehova Mulungu wako kuti ukwaniritse lonjezo lililonse, chifukwa zonsezo ndi zonyansa kwa Yehova Mulungu wako.
6 “Musamapatse agalu zinthu zopatulika,+ kapena kuponyera nkhumba ngale zanu, kuopera kuti zingapondeponde ngalezo+ kenako n’kutembenuka ndi kukukhadzulani.
2 Chenjerani ndi agalu.+ Chenjerani ndi ochita ntchito zovulaza. Chenjerani ndi anthu amene amachita mdulidwe.+