Genesis 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo anali kufuula kwa Loti kuti: “Kodi amuna amene abwera usiku uno aja, ali kuti? Atulutse kuti tigone nawo.”+ Aroma 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Amunanso chimodzimodzi. Iwo anasiya njira yachibadwa yofuna akazi+ n’kumatenthetsana okhaokha mwachiwawa m’chilakolako choipa, amuna ndi amuna anzawo,+ kuchitirana zonyansa+ ndi kulandiriratu mphoto+ yoyenerera kulakwa kwawo.+ 1 Timoteyo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 adama,+ amuna ogonana ndi amuna anzawo, oba anthu, onama, olumbira monama,+ ndiponso ochita china chilichonse chosagwirizana+ ndi chiphunzitso cholondola.+ Chivumbulutso 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kunja kuli anthu amene ali ngati agalu,+ amene amachita zamizimu,+ adama,+ opha anthu, opembedza mafano, ndi aliyense wokonda kulankhula ndi kuchita zachinyengo.’+
5 Iwo anali kufuula kwa Loti kuti: “Kodi amuna amene abwera usiku uno aja, ali kuti? Atulutse kuti tigone nawo.”+
27 Amunanso chimodzimodzi. Iwo anasiya njira yachibadwa yofuna akazi+ n’kumatenthetsana okhaokha mwachiwawa m’chilakolako choipa, amuna ndi amuna anzawo,+ kuchitirana zonyansa+ ndi kulandiriratu mphoto+ yoyenerera kulakwa kwawo.+
10 adama,+ amuna ogonana ndi amuna anzawo, oba anthu, onama, olumbira monama,+ ndiponso ochita china chilichonse chosagwirizana+ ndi chiphunzitso cholondola.+
15 Kunja kuli anthu amene ali ngati agalu,+ amene amachita zamizimu,+ adama,+ opha anthu, opembedza mafano, ndi aliyense wokonda kulankhula ndi kuchita zachinyengo.’+