2 Timoteyo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gwiritsitsabe chitsanzo cha mawu olondola+ amene unawamva kwa ine, komanso chikhulupiriro ndi chikondi zomwe zili mwa Khristu Yesu.+ Tito 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi chiphunzitso cholondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa.
13 Gwiritsitsabe chitsanzo cha mawu olondola+ amene unawamva kwa ine, komanso chikhulupiriro ndi chikondi zomwe zili mwa Khristu Yesu.+
9 wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi chiphunzitso cholondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa.