1 Timoteyo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 adama,+ amuna ogonana ndi amuna anzawo, oba anthu, onama, olumbira monama,+ ndiponso ochita china chilichonse chosagwirizana+ ndi chiphunzitso cholondola.+ 2 Timoteyo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gwiritsitsabe chitsanzo cha mawu olondola+ amene unawamva kwa ine, komanso chikhulupiriro ndi chikondi zomwe zili mwa Khristu Yesu.+
10 adama,+ amuna ogonana ndi amuna anzawo, oba anthu, onama, olumbira monama,+ ndiponso ochita china chilichonse chosagwirizana+ ndi chiphunzitso cholondola.+
13 Gwiritsitsabe chitsanzo cha mawu olondola+ amene unawamva kwa ine, komanso chikhulupiriro ndi chikondi zomwe zili mwa Khristu Yesu.+