1 Timoteyo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 achiwerewere,* amuna amene amagonana ndi amuna anzawo, oba anthu, abodza, olumbira monama ndiponso ochita china chilichonse chosagwirizana ndi mfundo zolondola zimene Mulungu amaphunzitsa.+
10 achiwerewere,* amuna amene amagonana ndi amuna anzawo, oba anthu, abodza, olumbira monama ndiponso ochita china chilichonse chosagwirizana ndi mfundo zolondola zimene Mulungu amaphunzitsa.+