Aroma 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iwe amene umanena kuti “Usachite chigololo,”+ kodi umachitanso chigololo? Iweyo amene umalankhula zosonyeza kuti umanyansidwa ndi mafano, umabanso+ za mu akachisi kodi?
22 Iwe amene umanena kuti “Usachite chigololo,”+ kodi umachitanso chigololo? Iweyo amene umalankhula zosonyeza kuti umanyansidwa ndi mafano, umabanso+ za mu akachisi kodi?