Aroma 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti iye amene ali Myuda kunja kokha si Myuda ayi,+ ndiponso mdulidwe wakunja kokha wochitidwa pathupi, si mdulidwe ayi.+ Agalatiya 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tamverani! Ine Paulo, ndikukuuzani kuti mukadulidwa,+ Khristu sadzakhala waphindu kwa inu.
28 Pakuti iye amene ali Myuda kunja kokha si Myuda ayi,+ ndiponso mdulidwe wakunja kokha wochitidwa pathupi, si mdulidwe ayi.+