Yohane 8:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Poyankha iwo anati: “Atate wathu ndi Abulahamu.”+ Yesu anawauza kuti: “Ngati ndinu ana a Abulahamu,+ chitani ntchito za Abulahamu. Chivumbulutso 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Ndikudziwa masautso ako ndi umphawi wako, koma ndiwe wolemera.+ Ndikudziwanso za kutonza kwa odzitcha Ayudawo,+ pamene si Ayuda, koma ndiwo sunagoge wa Satana.+
39 Poyankha iwo anati: “Atate wathu ndi Abulahamu.”+ Yesu anawauza kuti: “Ngati ndinu ana a Abulahamu,+ chitani ntchito za Abulahamu.
9 ‘Ndikudziwa masautso ako ndi umphawi wako, koma ndiwe wolemera.+ Ndikudziwanso za kutonza kwa odzitcha Ayudawo,+ pamene si Ayuda, koma ndiwo sunagoge wa Satana.+