Chivumbulutso 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Ndikudziwa masautso ako ndi umphawi wako, koma ndiwe wolemera.+ Ndikudziwanso kuti pali anthu amene amanena kuti ndi Ayuda ndipo amakunyoza. Koma sikuti iwo ndi Ayuda, mʼmalomwake iwo ndi sunagoge wa Satana.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:9 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 38 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 1211/15/1989, ptsa. 22-234/1/1989, ptsa. 13-14
9 ‘Ndikudziwa masautso ako ndi umphawi wako, koma ndiwe wolemera.+ Ndikudziwanso kuti pali anthu amene amanena kuti ndi Ayuda ndipo amakunyoza. Koma sikuti iwo ndi Ayuda, mʼmalomwake iwo ndi sunagoge wa Satana.+
2:9 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 38 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 1211/15/1989, ptsa. 22-234/1/1989, ptsa. 13-14