Machitidwe 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno amuna ena ochokera ku Yudeya+ anapita kumeneko ndi kuyamba kuphunzitsa abale kuti: “Mukapanda kudulidwa+ malinga ndi mwambo wa Mose,+ simungapulumuke.” Agalatiya 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Onse ofuna kudzionetsa ngati abwino pamaso pa anthu ndi amene akukuumirizani kuti muzidulidwa.+ Akuchita zimenezi kuti asazunzidwe chifukwa cha mtengo wozunzikirapo wa Khristu,+ amene ndi Yesu.
15 Ndiyeno amuna ena ochokera ku Yudeya+ anapita kumeneko ndi kuyamba kuphunzitsa abale kuti: “Mukapanda kudulidwa+ malinga ndi mwambo wa Mose,+ simungapulumuke.”
12 Onse ofuna kudzionetsa ngati abwino pamaso pa anthu ndi amene akukuumirizani kuti muzidulidwa.+ Akuchita zimenezi kuti asazunzidwe chifukwa cha mtengo wozunzikirapo wa Khristu,+ amene ndi Yesu.