Agalatiya 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tamverani! Ine Paulo, ndikukuuzani kuti mukadulidwa,+ Khristu sadzakhala waphindu kwa inu.