Agalatiya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kunena za ine abale, ngati ndimalalikirabe kuti anthu azidulidwa, n’chifukwa chiyani ndikuzunzidwabe? Ndithudi, mtengo wozunzikirapo,+ womwe ndi chopunthwitsa,+ ukanakhala utachotsedwa.+ Afilipi 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti alipo ambiri amene ndinali kuwatchula kawirikawiri, koma tsopano ndikuwatchula ndi misozi, amene akuyenda monga adani a mtengo wozunzikirapo* wa Khristu.+
11 Kunena za ine abale, ngati ndimalalikirabe kuti anthu azidulidwa, n’chifukwa chiyani ndikuzunzidwabe? Ndithudi, mtengo wozunzikirapo,+ womwe ndi chopunthwitsa,+ ukanakhala utachotsedwa.+
18 Pakuti alipo ambiri amene ndinali kuwatchula kawirikawiri, koma tsopano ndikuwatchula ndi misozi, amene akuyenda monga adani a mtengo wozunzikirapo* wa Khristu.+