Tito 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kumene kwazikidwa pa chiyembekezo cha moyo wosatha,+ chomwe Mulungu amene sanganame,+ analonjeza kalekale.+ Chivumbulutso 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo wokhala pampando wachifumu+ anati: “Taonani! Zinthu zonse zimene ndikupanga n’zatsopano.”+ Ananenanso kuti: “Lemba, pakuti mawu awa ndi odalirika ndi oona.”
2 kumene kwazikidwa pa chiyembekezo cha moyo wosatha,+ chomwe Mulungu amene sanganame,+ analonjeza kalekale.+
5 Ndipo wokhala pampando wachifumu+ anati: “Taonani! Zinthu zonse zimene ndikupanga n’zatsopano.”+ Ananenanso kuti: “Lemba, pakuti mawu awa ndi odalirika ndi oona.”