Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 53:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chifukwa cha kuvutika kwake, iye adzaona zabwino+ ndipo adzakhutira.+ Chifukwa cha zimene akudziwa, mtumiki wanga wolungamayo+ adzachititsa kuti anthu ambiri azionedwa olungama,+ ndipo adzasenza zolakwa zawo.+

  • Aroma 16:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Tsopano Mulungu+ angakulimbitseni mwa uthenga wabwino umene ndikulengeza ndiponso mwa uthenga wonena za Yesu Khristu umene ukulalikidwa. Uthenga wabwino umenewu ndi wogwirizana ndi zimene zaululidwa zokhudza chinsinsi chopatulika+ chimene chakhala chobisika kuyambira nthawi zakale.

  • 2 Timoteyo 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Iye anatipulumutsa+ ndi kutiitana kuti tikhale oyera,+ osati chifukwa cha ntchito zathu,+ koma mwa chifuniro chake ndi kukoma mtima kwake kwakukulu. Iye anatikomera mtima m’njira imeneyi kalekalelo mwa Khristu Yesu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena