Aefeso 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 moti anatiululira chinsinsi chopatulika+ cha chifuniro chake. Chinsinsicho n’chogwirizana ndi zokomera mwiniwakeyo ndiponso zimene anafuna mumtima mwake,+ Aefeso 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ndiponso kuti ndionetse anthu mmene chinsinsi chopatulikacho+ chikuyendetsedwera.+ Kuyambira kalekale, chinsinsi chimenechi chakhala chobisika mwa —Mulungu, amene analenga zinthu zonse.+ Akolose 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mawuwo ndi chinsinsi chopatulika+ chimene chinabisidwa nthawi* zakale,+ ndiponso kwa mibadwo yakale. Koma tsopano chaululidwa+ kwa oyera ake.
9 moti anatiululira chinsinsi chopatulika+ cha chifuniro chake. Chinsinsicho n’chogwirizana ndi zokomera mwiniwakeyo ndiponso zimene anafuna mumtima mwake,+
9 ndiponso kuti ndionetse anthu mmene chinsinsi chopatulikacho+ chikuyendetsedwera.+ Kuyambira kalekale, chinsinsi chimenechi chakhala chobisika mwa —Mulungu, amene analenga zinthu zonse.+
26 Mawuwo ndi chinsinsi chopatulika+ chimene chinabisidwa nthawi* zakale,+ ndiponso kwa mibadwo yakale. Koma tsopano chaululidwa+ kwa oyera ake.