Aefeso 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’mibadwo ina, chinsinsi+ chimenechi sichinaululidwe kwa ana a anthu mmene chaululidwira+ tsopano kwa atumwi ndi aneneri+ ake oyera mwa mzimu. Aefeso 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chinsinsi chopatulika+ chimenechi n’chachikulu. Tsopano ndikulankhula za Khristu ndi mpingo.+
5 M’mibadwo ina, chinsinsi+ chimenechi sichinaululidwe kwa ana a anthu mmene chaululidwira+ tsopano kwa atumwi ndi aneneri+ ake oyera mwa mzimu.