Mateyu 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Yesu anamuuza kuti: “Ndiwe wodala Simoni mwana wa Yona, chifukwa si munthu* amene wakuululira zimenezi, koma Atate wanga amene ali kumwamba wachita zimenezi.+ Aefeso 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwamangidwa pamaziko+ a atumwi+ ndi aneneri,+ ndipo Khristu Yesuyo ndiye mwala wapakona wa mazikowo.+
17 Pamenepo Yesu anamuuza kuti: “Ndiwe wodala Simoni mwana wa Yona, chifukwa si munthu* amene wakuululira zimenezi, koma Atate wanga amene ali kumwamba wachita zimenezi.+
20 Mwamangidwa pamaziko+ a atumwi+ ndi aneneri,+ ndipo Khristu Yesuyo ndiye mwala wapakona wa mazikowo.+