Aefeso 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 moti anatiululira chinsinsi chopatulika+ cha chifuniro chake. Chinsinsicho n’chogwirizana ndi zokomera mwiniwakeyo ndiponso zimene anafuna mumtima mwake,+ Aefeso 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa chifukwa chimenechi, inuyo mukawerenga zimenezi mutha kuzindikira kuti chinsinsi chopatulika+ chonena za Khristu ndikuchimvetsa bwino.+ Akolose 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mawuwo ndi chinsinsi chopatulika+ chimene chinabisidwa nthawi* zakale,+ ndiponso kwa mibadwo yakale. Koma tsopano chaululidwa+ kwa oyera ake.
9 moti anatiululira chinsinsi chopatulika+ cha chifuniro chake. Chinsinsicho n’chogwirizana ndi zokomera mwiniwakeyo ndiponso zimene anafuna mumtima mwake,+
4 Pa chifukwa chimenechi, inuyo mukawerenga zimenezi mutha kuzindikira kuti chinsinsi chopatulika+ chonena za Khristu ndikuchimvetsa bwino.+
26 Mawuwo ndi chinsinsi chopatulika+ chimene chinabisidwa nthawi* zakale,+ ndiponso kwa mibadwo yakale. Koma tsopano chaululidwa+ kwa oyera ake.