1 Akorinto 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero anthu azitha kuona kuti ndife atumiki+ a Khristu ndi oyang’anira+ zinsinsi zopatulika+ za Mulungu. Aefeso 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 kuphatikizapo ineyo. Chitani zimenezi kuti ndikatsegula pakamwa panga kuti ndilankhule, ndizitha kulankhula+ mwaufulu+ kuti ndidziwitse ena chinsinsi chopatulika cha uthenga wabwino,+
4 Chotero anthu azitha kuona kuti ndife atumiki+ a Khristu ndi oyang’anira+ zinsinsi zopatulika+ za Mulungu.
19 kuphatikizapo ineyo. Chitani zimenezi kuti ndikatsegula pakamwa panga kuti ndilankhule, ndizitha kulankhula+ mwaufulu+ kuti ndidziwitse ena chinsinsi chopatulika cha uthenga wabwino,+