Aefeso 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Muzindipemphereranso ineyo kuti ndikayamba kulankhula ndizipeza mawu oyenerera nʼcholinga choti ndizitha kulankhula molimba mtima ndikamalalikira zokhudza chinsinsi chopatulika cha uthenga wabwino,+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:19 Nsanja ya Olonda,5/15/2006, tsa. 14
19 Muzindipemphereranso ineyo kuti ndikayamba kulankhula ndizipeza mawu oyenerera nʼcholinga choti ndizitha kulankhula molimba mtima ndikamalalikira zokhudza chinsinsi chopatulika cha uthenga wabwino,+