Akolose 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komanso muzitipempherera ifeyo+ kuti Mulungu atitsegulire khomo kuti tithe kulalikira mawu ndi kulankhula za chinsinsi chopatulika chokhudza Khristu, chimene chinachititsa kuti ndimangidwe nʼkukhala mʼndende muno,+
3 Komanso muzitipempherera ifeyo+ kuti Mulungu atitsegulire khomo kuti tithe kulalikira mawu ndi kulankhula za chinsinsi chopatulika chokhudza Khristu, chimene chinachititsa kuti ndimangidwe nʼkukhala mʼndende muno,+