Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aefeso 6:19, 20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Muzindipemphereranso ineyo kuti ndikayamba kulankhula ndizipeza mawu oyenerera nʼcholinga choti ndizitha kulankhula molimba mtima ndikamalalikira zokhudza chinsinsi chopatulika cha uthenga wabwino,+ 20 umene ndine kazembe+ wake womangidwa ndi unyolo ndiponso kuti ndilankhule za uthengawo molimba mtima ngati mmene ndikuyenera kuchitira.

  • Afilipi 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Nʼzoyenera kwa ine kuti ndiganizire nonsenu mwa njira imeneyi, chifukwa ndinu apamtima panga. Inu amene munandithandiza pa nthawi imene ndinamangidwa maunyolo mʼndende+ komanso poteteza uthenga wabwino ndi kukhazikitsa mwalamulo ntchito yolengeza uthenga wabwino.+ Inu limodzi ndi ine tinapindula ndi kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena