Akolose 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mawuwo akuphatikizapo chinsinsi chopatulika+ chimene dziko silinachidziwe+ ndiponso chinali chobisika kwa mibadwo yakale. Koma tsopano chaululidwa kwa oyera ake.+ Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:26 Nsanja ya Olonda,12/15/1994, ptsa. 12-13
26 Mawuwo akuphatikizapo chinsinsi chopatulika+ chimene dziko silinachidziwe+ ndiponso chinali chobisika kwa mibadwo yakale. Koma tsopano chaululidwa kwa oyera ake.+