Aefeso 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 kuti akakhazikitse dongosolo+ lake, ikadzatha nyengo yonse ya nthawi zoikidwiratu.+ Dongosolo limenelo ndilo kusonkhanitsanso+ zinthu zonse pamodzi mwa Khristu,+ zinthu zakumwamba+ ndi zinthu zapadziko lapansi.+ Inde, kuzisonkhanitsanso mwa iye. Akolose 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye ndiyenso mutu wa thupilo, lomwe ndi mpingo.+ Iye ndiye chiyambi, woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,+ kuti adzakhale woyamba+ pa zinthu zonse.
10 kuti akakhazikitse dongosolo+ lake, ikadzatha nyengo yonse ya nthawi zoikidwiratu.+ Dongosolo limenelo ndilo kusonkhanitsanso+ zinthu zonse pamodzi mwa Khristu,+ zinthu zakumwamba+ ndi zinthu zapadziko lapansi.+ Inde, kuzisonkhanitsanso mwa iye.
18 Iye ndiyenso mutu wa thupilo, lomwe ndi mpingo.+ Iye ndiye chiyambi, woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,+ kuti adzakhale woyamba+ pa zinthu zonse.