Luka 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Anthu adzaphedwa ndi lupanga ndiponso kutengedwa ukapolo kupita nawo ku mitundu ina yonse.+ Anthu a mitundu ina adzapondaponda Yerusalemu, kufikira nthawi zoikidwiratu+ za anthu a mitundu inawo zitakwanira. Machitidwe 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anawayankha kuti: “Si kwa inu kudziwa nthawi kapena nyengo+ zimene Atate waziika pansi pa ulamuliro wake.+
24 Anthu adzaphedwa ndi lupanga ndiponso kutengedwa ukapolo kupita nawo ku mitundu ina yonse.+ Anthu a mitundu ina adzapondaponda Yerusalemu, kufikira nthawi zoikidwiratu+ za anthu a mitundu inawo zitakwanira.
7 Iye anawayankha kuti: “Si kwa inu kudziwa nthawi kapena nyengo+ zimene Atate waziika pansi pa ulamuliro wake.+