10 zoti akakhazikitse dongosolo lake pa nthawi imene anaikiratu. Dongosolo limenelo ndi kusonkhanitsa zinthu zonse pamodzi kuti zikhale zogwirizana ndi Khristu, zinthu zakumwamba ndi zinthu zapadziko lapansi.+ Inde, zinthu zonse zidzasonkhanitsidwa kwa Khristu,