CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AEFESO 1-3
Zimene Ulamuliro wa Yehova Ukuchita
Ulamuliro wa Yehova ukugwirizanitsa anthu komanso angelo.
Ukukonzekeretsa Akhristu odzozedwa kuti akalamulire kumwamba motsogoleredwa ndi Yesu Khristu
Ukukonzekeretsa anthu omwe adzakhale padziko lapansi n’kumalamuliridwa ndi Ufumu wa Mesiya
Kodi ndi zinthu ziti zomwe ndingachite pothandiza kuti tizikhala ogwirizana m’gulu la Yehova?