June Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya June 2019 Zimene Tinganene June 3-9 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AGALATIYA 4-6 Nkhani ‘Yophiphiritsira’ Yomwe ndi Yofunika Kwambiri kwa Ife June 10-16 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AEFESO 1-3 Zimene Ulamuliro wa Yehova Ukuchita MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzipindula Mokwanira Mukamaphunzira Panokha June 17-23 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AEFESO 4-6 “Valani Zida Zonse Zankhondo Zochokera kwa Mulungu” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Maganizo a Yehova Ndi Otani pa Nkhaniyi? June 24-30 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AFILIPI 1-4 “Musamade Nkhawa ndi Kanthu Kalikonse” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mumasankha Zosangalatsa Mwanzeru?