Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 June tsamba 6
  • June 24-30

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 24-30
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 June tsamba 6

June 24-30

AFILIPI 1-4

  • Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Musamade Nkhawa ndi Kanthu Kalikonse”: (10 min.)

    • [Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Afilipi.]

    • Afil. 4:6​—Mukakhala ndi nkhawa muzipemphera kwa Yehova (w17.08 10 ¶10)

    • Afil. 4:7​—Muzilola kuti “mtendere wa Mulungu” uzikutetezani (w17.08 10 ¶7; 12 ¶16)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Afil. 2:17​—Kodi mtumwi Paulo ‘anadzipereka ngati nsembe yachakumwa’ m’njira yotani? (it-2 528 ¶5)

    • Afil. 3:11​—Kodi “kuuka koyambirira” kumatanthauza chiyani? (w07 1/1 26-27 ¶5)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Afil. 4:10-23 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 4)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) fg phunziro 6 ¶3-4 (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 45

  • Kodi Zipangizo Zanu Zamakono Zimakulamulirani?: (5 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako kambiranani mafunso awa: Kodi zipangizo zamakono ndi zothandiza bwanji? Kodi tingakumane ndi mavuto otani ngati nthawi zonse timangokhalira kugwiritsa ntchito zipangizozi? Nanga mungadziwe bwanji ngati muli ndi vutoli? N’chiyani chingakuthandizeni kuti nthawi zonse muzichita “zinthu zofunika kwambiri”? (Afil. 1:10)

  • “Kodi Mumasankha Zosangalatsa Mwanzeru?”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kodi Ndiyenera Kusankha Zosangalatsa Zotani?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 41

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 32 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena