Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 June tsamba 2
  • June 3-9

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 3-9
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 June tsamba 2

June 3-9

AGALATIYA 4-6

  • Nyimbo Na. 16 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Nkhani ‘Yophiphiritsira’ Yomwe ndi Yofunika Kwambiri kwa Ife”: (10 min.)

    • Agal. 4:24, 25​—Hagara ankaimira mtundu wa Isiraeli womwe unkatsatira Chilamulo (it-1 1018 ¶2)

    • Agal. 4:26, 27​—Sara ankaimira “Yerusalemu wam’mwamba,” yemwe ndi mbali yakumwamba ya gulu la Yehova (w14 10/15 10 ¶11)

    • Agal. 4:28-31​—Anthu omvera adzadalitsidwa kudzera mwa “ana” a Yerusalemu wam’mwamba

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Agal. 4:6​—Kodi mawu achiheberi kapena achialamu akuti abba, amatanthauza chiyani? (w09 4/1 13)

    • Agal. 6:17​—Kodi n’kutheka kuti mtumwi Paulo ankatanthauza chiyani ponena kuti thupi lake linali ndi “zipsera za chizindikiro cha kapolo wa Yesu?” (w10 11/1 15)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Agal. 4:1-20 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kufotokoza Bwino Malemba, kenako kambiranani phunziro 6 m’kabuku ka Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w12 3/15 30-31​—Mutu: N’chifukwa Chiyani Akhristu Ayenera Kupeweratu Kuwonera Zolaula? (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 110

  • Zofunika Pampingo: (8 min.)

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onetsani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya June.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 38

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 147 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena