1 Akorinto 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma zinthu zonse zikadzakhala pansi pake,+ Mwanayonso adzadziika pansi pa amene+ anaika zinthu zonse pansi pake, kuti Mulungu akhale zinthu zonse kwa aliyense.+ Akolose 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kuti kudzera mwa mwana wakeyo iye agwirizanitsenso+ zinthu zina zonse ndi iyeyo,+ pokhazikitsa mtendere+ mwa magazi+ amene iye anakhetsa pamtengo wozunzikirapo,*+ kaya zikhale zinthu zapadziko lapansi kapena zinthu zakumwamba.
28 Koma zinthu zonse zikadzakhala pansi pake,+ Mwanayonso adzadziika pansi pa amene+ anaika zinthu zonse pansi pake, kuti Mulungu akhale zinthu zonse kwa aliyense.+
20 Kuti kudzera mwa mwana wakeyo iye agwirizanitsenso+ zinthu zina zonse ndi iyeyo,+ pokhazikitsa mtendere+ mwa magazi+ amene iye anakhetsa pamtengo wozunzikirapo,*+ kaya zikhale zinthu zapadziko lapansi kapena zinthu zakumwamba.