Aefeso 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 kuti akakhazikitse dongosolo+ lake, ikadzatha nyengo yonse ya nthawi zoikidwiratu.+ Dongosolo limenelo ndilo kusonkhanitsanso+ zinthu zonse pamodzi mwa Khristu,+ zinthu zakumwamba+ ndi zinthu zapadziko lapansi.+ Inde, kuzisonkhanitsanso mwa iye.
10 kuti akakhazikitse dongosolo+ lake, ikadzatha nyengo yonse ya nthawi zoikidwiratu.+ Dongosolo limenelo ndilo kusonkhanitsanso+ zinthu zonse pamodzi mwa Khristu,+ zinthu zakumwamba+ ndi zinthu zapadziko lapansi.+ Inde, kuzisonkhanitsanso mwa iye.