Aefeso 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ndiponso kuti ndithandize aliyense kuti aone mmene chinsinsi chopatulikacho+ chikuyendetsedwera. Kwa zaka zambiri, Mulungu amene analenga zinthu zonse, wakhala akubisa chinsinsi chimenechi.
9 ndiponso kuti ndithandize aliyense kuti aone mmene chinsinsi chopatulikacho+ chikuyendetsedwera. Kwa zaka zambiri, Mulungu amene analenga zinthu zonse, wakhala akubisa chinsinsi chimenechi.