-
Aefeso 1:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 potiululira chinsinsi chake chopatulika+ chokhudza chifuniro chake. Chinsinsicho nʼchogwirizana ndi zimene zimamusangalatsa ndiponso zimene amafuna, 10 zoti akakhazikitse dongosolo lake pa nthawi imene anaikiratu. Dongosolo limenelo ndi kusonkhanitsa zinthu zonse pamodzi kuti zikhale zogwirizana ndi Khristu, zinthu zakumwamba ndi zinthu zapadziko lapansi.+ Inde, zinthu zonse zidzasonkhanitsidwa kwa Khristu,
-