20 Tsopano kwa iye amene angathe kuchita zazikulu kwambiri kuposa zonse zimene timapempha kapena kuganiza,+ malinga ndi mphamvu yake imene ikugwira ntchito+ mwa ife,
24 Koma ponena za Mulungu amene angathe kukutetezani+ kuti musapunthwe, ndiponso kukuikani opanda chilema+ pamaso pa ulemerero wake ndi chisangalalo chachikulu,