Maliko 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 N’chifukwa chake ndikukuuzani kuti, Pa zinthu zonse zimene mukupempherera ndi kupempha, khalani ndi chikhulupiriro ngati kuti mwazilandira kale, ndipo mudzazilandiradi.+ 1 Akorinto 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma monga mmene Malemba amanenera: “Palibe munthu amene anaonapo kapena kumvapo kapenanso kuganizapo zimene Mulungu wakonzera omukonda.”+
24 N’chifukwa chake ndikukuuzani kuti, Pa zinthu zonse zimene mukupempherera ndi kupempha, khalani ndi chikhulupiriro ngati kuti mwazilandira kale, ndipo mudzazilandiradi.+
9 Koma monga mmene Malemba amanenera: “Palibe munthu amene anaonapo kapena kumvapo kapenanso kuganizapo zimene Mulungu wakonzera omukonda.”+