1 Akorinto 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma mogwirizana ndi zimene Malemba amanena: “Palibe munthu amene anaonapo kapena kumva kapenanso kuganiza zimene Mulungu wakonzera anthu amene amamukonda.”+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:9 Yesaya 2, tsa. 366 Nsanja ya Olonda,12/1/1989, tsa. 22
9 Koma mogwirizana ndi zimene Malemba amanena: “Palibe munthu amene anaonapo kapena kumva kapenanso kuganiza zimene Mulungu wakonzera anthu amene amamukonda.”+