Yesaya 64:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuyambira kalekale palibe amene anamvapo, kuganizira,Kapena kuona Mulungu wina kupatulapo inu,Amene mumathandiza anthu omwe amayembekezera inu moleza mtima.+
4 Kuyambira kalekale palibe amene anamvapo, kuganizira,Kapena kuona Mulungu wina kupatulapo inu,Amene mumathandiza anthu omwe amayembekezera inu moleza mtima.+