Yesaya 64:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuyambira kalekale palibe amene anamvapo+ kapena kuganizira za Mulungu wina kupatula inu,+ ndipo palibe amene anamuonapo. Inu mumathandiza munthu amene akukuyembekezerani.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 64:4 Yesaya 2, tsa. 364
4 Kuyambira kalekale palibe amene anamvapo+ kapena kuganizira za Mulungu wina kupatula inu,+ ndipo palibe amene anamuonapo. Inu mumathandiza munthu amene akukuyembekezerani.+