Yesaya 64:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuyambira kalekale palibe amene anamvapo, kuganizira,Kapena kuona Mulungu wina kupatulapo inu,Amene mumathandiza anthu omwe amayembekezera inu moleza mtima.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 64:4 Yesaya 2, tsa. 364
4 Kuyambira kalekale palibe amene anamvapo, kuganizira,Kapena kuona Mulungu wina kupatulapo inu,Amene mumathandiza anthu omwe amayembekezera inu moleza mtima.+