Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Pemphanibe,+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna, ndipo mudzapeza. Gogodanibe,+ ndipo adzakutsegulirani.

  • Mateyu 18:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndiponso ndikukuuzani kuti, ngati awiri mwa inu padziko lapansi pano adzagwirizana pa chilichonse chofunika kupempha, Atate wanga wakumwamba adzawachitira.+

  • Mateyu 21:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Chinthu chilichonse chimene mudzapempha m’mapemphero anu, mudzalandira ngati muli ndi chikhulupiriro.”+

  • Luka 11:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Choncho ndikukuuzani, Pemphanibe,+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna,+ ndipo mudzapeza. Gogodanibe, ndipo adzakutsegulirani.

  • Yohane 14:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Komanso chilichonse chimene mudzapemphe m’dzina langa, ine ndidzachichita, kuti Atate alemekezedwe mwa Mwana wake.+

  • Yohane 15:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ngati mukhala ogwirizana ndi ine ndipo mawu anga akakhala mwa inu, mukhoza kupempha chilichonse chimene mukufuna ndipo chidzachitika kwa inu.+

  • Yohane 16:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kufikira nthawi ino simunapemphepo chilichonse m’dzina langa. Pemphani ndipo mudzalandira, kuti chimwemwe chanu chisefukire.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena