Yohane 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inu simunandisankhe ine, koma ine ndinakusankhani. Ndinakuikani kuti mupitirize kubala zipatso zochuluka,+ ndi kutinso zipatso zanuzo zisathe, kuti chilichonse chimene mungapemphe Atate m’dzina langa akupatseni.+ Yohane 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pa tsiku limenelo+ simudzandifunsanso mafunso. Ndithudi ndikukuuzani, Ngati mupempha chilichonse+ kwa Atate m’dzina langa adzakupatsani.+
16 Inu simunandisankhe ine, koma ine ndinakusankhani. Ndinakuikani kuti mupitirize kubala zipatso zochuluka,+ ndi kutinso zipatso zanuzo zisathe, kuti chilichonse chimene mungapemphe Atate m’dzina langa akupatseni.+
23 Pa tsiku limenelo+ simudzandifunsanso mafunso. Ndithudi ndikukuuzani, Ngati mupempha chilichonse+ kwa Atate m’dzina langa adzakupatsani.+