-
Yohane 16:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Mpaka pano simunapemphepo chilichonse mʼdzina langa. Pemphani ndipo mudzalandira kuti chimwemwe chanu chisefukire.
-